Numeri 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Manawo+ anali ngati mapira,*+ ndipo ankaoneka ngati utomoni woonekera mkati ngati galasi.