Numeri 11:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngati izi ndi zimene muzindichitira kuli bwino mungondipha pompano.+ Koma ngati mwandikomera mtima, musandionetsenso tsoka lina.”
15 Ngati izi ndi zimene muzindichitira kuli bwino mungondipha pompano.+ Koma ngati mwandikomera mtima, musandionetsenso tsoka lina.”