Numeri 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova anayankha Mose kuti: “Undisonkhanitsire akulu 70 pakati pa akulu a Isiraeli, amene umawaona* kuti ndi akulu komanso oyangʼanira pakati pa anthuwo.+ Upite nawo kuchihema chokumanako, ndipo akaime kumeneko limodzi ndi iwe.
16 Yehova anayankha Mose kuti: “Undisonkhanitsire akulu 70 pakati pa akulu a Isiraeli, amene umawaona* kuti ndi akulu komanso oyangʼanira pakati pa anthuwo.+ Upite nawo kuchihema chokumanako, ndipo akaime kumeneko limodzi ndi iwe.