Numeri 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthuwo uwauze kuti, ‘Mudziyeretse pokonzekera mawa,+ chifukwa mudya nyama. Paja mwakhala mukulirira Yehova+ kuti: “Ndani atipatse nyama yoti tidye? Ku Iguputo zinthu zinkatiyendera bwino.”+ Yehova akupatsanidi nyamayo ndipo mudya.+
18 Anthuwo uwauze kuti, ‘Mudziyeretse pokonzekera mawa,+ chifukwa mudya nyama. Paja mwakhala mukulirira Yehova+ kuti: “Ndani atipatse nyama yoti tidye? Ku Iguputo zinthu zinkatiyendera bwino.”+ Yehova akupatsanidi nyamayo ndipo mudya.+