Numeri 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndiyeno anthuwo anayamba kugwira zinzirizo. Anazigwira masana onse, usiku wonse, mpakanso tsiku lotsatira osapuma. Palibe amene anagwira zosakwana mahomeri* 10 ndipo ankaziyanika paliponse, moti zinangoti mbwee, pamsasa wonsewo.
32 Ndiyeno anthuwo anayamba kugwira zinzirizo. Anazigwira masana onse, usiku wonse, mpakanso tsiku lotsatira osapuma. Palibe amene anagwira zosakwana mahomeri* 10 ndipo ankaziyanika paliponse, moti zinangoti mbwee, pamsasa wonsewo.