Numeri 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Anthuwo atachoka pa Kibiroti-hatava, anasamukira ku Hazeroti,+ ndipo anakhala kumeneko.