Numeri 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Yehova anatsika mʼchipilala chamtambo+ nʼkuima pakhomo la chihema chokumanako. Kenako anaitana Aroni ndi Miriamu ndipo onse anapita.
5 Ndiyeno Yehova anatsika mʼchipilala chamtambo+ nʼkuima pakhomo la chihema chokumanako. Kenako anaitana Aroni ndi Miriamu ndipo onse anapita.