Numeri 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Utume amuna kuti akazonde* dziko la Kanani limene ndikulipereka kwa Aisiraeli. Pa fuko lililonse utume mwamuna mmodzi, ndipo akhale mtsogoleri+ wa fuko lawo.”+
2 “Utume amuna kuti akazonde* dziko la Kanani limene ndikulipereka kwa Aisiraeli. Pa fuko lililonse utume mwamuna mmodzi, ndipo akhale mtsogoleri+ wa fuko lawo.”+