Numeri 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Powatumiza kuti akazonde dziko la Kanani, Mose anawauza kuti: “Mupite kumeneko kudzera ku Negebu, ndipo kenako mukafike kudera lamapiri.+
17 Powatumiza kuti akazonde dziko la Kanani, Mose anawauza kuti: “Mupite kumeneko kudzera ku Negebu, ndipo kenako mukafike kudera lamapiri.+