Numeri 13:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ngakhale zili choncho, anthu okhala kumeneko ndi anthu amphamvu zawo, ndipo ali ndi mizinda ikuluikulu yotchingidwa ndi mipanda yolimba kwambiri. Si zokhazo, taonanso Aanaki kumeneko.+
28 Ngakhale zili choncho, anthu okhala kumeneko ndi anthu amphamvu zawo, ndipo ali ndi mizinda ikuluikulu yotchingidwa ndi mipanda yolimba kwambiri. Si zokhazo, taonanso Aanaki kumeneko.+