Numeri 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tinaonakonso Anefili,* ana a Anaki+ omwe ndi mbadwa za Anefili, moti tikadziyerekezera ndi iwowo, ifeyo timangooneka ngati tiziwala. Iwonso ndi mmene amationera.” Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:33 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,7/15/2011, ptsa. 10-1110/1/2006, tsa. 16
33 Tinaonakonso Anefili,* ana a Anaki+ omwe ndi mbadwa za Anefili, moti tikadziyerekezera ndi iwowo, ifeyo timangooneka ngati tiziwala. Iwonso ndi mmene amationera.”