Numeri 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiponso muzikapereka vinyo kuti akhale nsembe yachakumwa. Azikakhala wokwana gawo limodzi mwa magawo atatu a muyezo wa hini, kuti akhale nsembe yakafungo kosangalatsa* kwa Yehova.
7 Ndiponso muzikapereka vinyo kuti akhale nsembe yachakumwa. Azikakhala wokwana gawo limodzi mwa magawo atatu a muyezo wa hini, kuti akhale nsembe yakafungo kosangalatsa* kwa Yehova.