Numeri 15:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma munthu amene wachita tchimo mwadala,+ kaya akhale nzika kapena mlendo, ndiye kuti wanyoza Yehova ndipo ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu ake.
30 Koma munthu amene wachita tchimo mwadala,+ kaya akhale nzika kapena mlendo, ndiye kuti wanyoza Yehova ndipo ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu ake.