Numeri 15:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 ‘Zovala zanu zizikhala ndi ulusi kuti mukaziona muzikumbukira malamulo onse a Yehova ndi kuwasunga.+ Musamatsatire zilakolako za mitima yanu ndi maso anu, chifukwa nʼzimene zikukupangitsani kuti musakhale okhulupirika kwa ine.*+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:39 Nsanja ya Olonda,7/15/2011, ptsa. 12-137/15/2003, tsa. 13
39 ‘Zovala zanu zizikhala ndi ulusi kuti mukaziona muzikumbukira malamulo onse a Yehova ndi kuwasunga.+ Musamatsatire zilakolako za mitima yanu ndi maso anu, chifukwa nʼzimene zikukupangitsani kuti musakhale okhulupirika kwa ine.*+