Numeri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi mukuyesa nʼchinthu chachingʼono kuti Mulungu wa Isiraeli anakupatulani pakati pa Aisiraeli,+ nʼkukulolani kuti muzifika pamaso pa Yehova kuti muzimutumikira pachihema chake komanso kutumikira gulu lonselo?+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:9 Nsanja ya Olonda,8/1/2000, ptsa. 10-11
9 Kodi mukuyesa nʼchinthu chachingʼono kuti Mulungu wa Isiraeli anakupatulani pakati pa Aisiraeli,+ nʼkukulolani kuti muzifika pamaso pa Yehova kuti muzimutumikira pachihema chake komanso kutumikira gulu lonselo?+