Numeri 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha zimene mukuchitazi, iweyo limodzi ndi anthu onse amene akukutsatira, mukuukira Yehova. Kunena za Aroni, kodi iyeyo ndi ndani kuti mumudandaule?”+
11 Chifukwa cha zimene mukuchitazi, iweyo limodzi ndi anthu onse amene akukutsatira, mukuukira Yehova. Kunena za Aroni, kodi iyeyo ndi ndani kuti mumudandaule?”+