-
Numeri 16:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Aliyense adzatenge chofukizira chake nʼkuikamo zofukiza, ndipo aliyense adzabweretse chofukizira chake pamaso pa Yehova. Zofukizirazo zidzakhale zokwana 250, komanso iweyo ndi Aroni aliyense adzakhale ndi chake.”
-