Numeri 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kora atasonkhanitsa anthu onse omutsatira+ kuti atsutsane nawo pakhomo la chihema chokumanako, ulemerero wa Yehova unaonekera ku gulu lonselo.+
19 Kora atasonkhanitsa anthu onse omutsatira+ kuti atsutsane nawo pakhomo la chihema chokumanako, ulemerero wa Yehova unaonekera ku gulu lonselo.+