Numeri 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nthakayo inangʼambika* nʼkuwameza limodzi ndi mabanja awo komanso anthu ena onse amene anali kumbali ya Kora+ pamodzi ndi katundu wawo yense.
32 Nthakayo inangʼambika* nʼkuwameza limodzi ndi mabanja awo komanso anthu ena onse amene anali kumbali ya Kora+ pamodzi ndi katundu wawo yense.