-
Numeri 16:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Choncho wansembe Eleazara anatenga zofukizira zakopa zimene anthu amene anapsa ndi moto aja anabweretsa, ndipo anazisula nʼkupanga timalata tokutira guwa lansembe,
-