Numeri 16:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Anthuwo anasonkhana pamodzi kuti aukire Mose ndi Aroni, kenako anatembenuka nʼkuyangʼana kuchihema chokumanako. Atatero anangoona kuti mtambo waphimba chihemacho ndipo ulemerero wa Yehova wayamba kuonekera.+
42 Anthuwo anasonkhana pamodzi kuti aukire Mose ndi Aroni, kenako anatembenuka nʼkuyangʼana kuchihema chokumanako. Atatero anangoona kuti mtambo waphimba chihemacho ndipo ulemerero wa Yehova wayamba kuonekera.+