Numeri 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Iwe ndi ana ako, ndi nyumba yonse ya bambo ako, mudzayankha mlandu wa zolakwa zanu pa malamulo okhudza malo opatulika.+ Iweyo ndi ana ako mudzayankha mlandu wa zolakwa zanu pa malamulo okhudza unsembe wanu.+
18 Kenako Yehova anauza Aroni kuti: “Iwe ndi ana ako, ndi nyumba yonse ya bambo ako, mudzayankha mlandu wa zolakwa zanu pa malamulo okhudza malo opatulika.+ Iweyo ndi ana ako mudzayankha mlandu wa zolakwa zanu pa malamulo okhudza unsembe wanu.+