Numeri 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndatenga Alevi omwe ndi abale anu pakati pa Aisiraeli ndipo ndawapereka kwa inu kuti akhale mphatso yanu.+ Iwo aperekedwa kwa Yehova kuti azitumikira pachihema chokumanako.+
6 Ine ndatenga Alevi omwe ndi abale anu pakati pa Aisiraeli ndipo ndawapereka kwa inu kuti akhale mphatso yanu.+ Iwo aperekedwa kwa Yehova kuti azitumikira pachihema chokumanako.+