Numeri 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ili ndi lamulo limene Yehova wapereka, ‘Uzani Aisiraeli kuti akupatseni ngʼombe yaikazi yofiira, yathanzi komanso yopanda chilema+ yomwe sinamangidwepo goli.
2 “Ili ndi lamulo limene Yehova wapereka, ‘Uzani Aisiraeli kuti akupatseni ngʼombe yaikazi yofiira, yathanzi komanso yopanda chilema+ yomwe sinamangidwepo goli.