Numeri 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Akatha, wansembeyo achape zovala zake nʼkusamba* ndi madzi. Pambuyo pake akhoza kulowa mumsasa, koma adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.
7 Akatha, wansembeyo achape zovala zake nʼkusamba* ndi madzi. Pambuyo pake akhoza kulowa mumsasa, koma adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.