Numeri 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Limeneli likhale lamulo kwa iwo mpaka kalekale: Munthu amene anawaza madzi oyeretsera,+ azichapa zovala zake. Ndipo munthu amene angakhudze madzi oyeretserawo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.
21 Limeneli likhale lamulo kwa iwo mpaka kalekale: Munthu amene anawaza madzi oyeretsera,+ azichapa zovala zake. Ndipo munthu amene angakhudze madzi oyeretserawo azikhala wodetsedwa mpaka madzulo.