Numeri 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthuwo anayamba kukangana ndi Mose+ kuti: “Zikanakhala bwino tikanangofera limodzi ndi abale athu aja amene anafa pamaso pa Yehova. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:3 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),2/2019, ptsa. 12-13
3 Anthuwo anayamba kukangana ndi Mose+ kuti: “Zikanakhala bwino tikanangofera limodzi ndi abale athu aja amene anafa pamaso pa Yehova.