Numeri 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nʼchifukwa chiyani munatitulutsa mʼdziko la Iguputo nʼkutibweretsa kumalo oipa ano?+ Kuno sikungamere mbewu iliyonse ndipo kulibe mitengo ya nkuyu, mitengo ya mpesa kapena mitengo ya makangaza. Ndi madzi akumwa omwe kulibe.”+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:5 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),2/2019, ptsa. 12-13 Nsanja ya Olonda,9/1/2009, tsa. 19
5 Nʼchifukwa chiyani munatitulutsa mʼdziko la Iguputo nʼkutibweretsa kumalo oipa ano?+ Kuno sikungamere mbewu iliyonse ndipo kulibe mitengo ya nkuyu, mitengo ya mpesa kapena mitengo ya makangaza. Ndi madzi akumwa omwe kulibe.”+