Numeri 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mose atatero, anakweza dzanja lake nʼkumenya thanthwelo kawiri ndi ndodo yake. Ndiyeno madzi ambiri anayamba kutuluka ndipo gulu lonselo linayamba kumwa madziwo limodzi ndi ziweto zawo.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:11 Nsanja ya Olonda,9/1/2009, tsa. 1910/15/1987, ptsa. 30-31
11 Mose atatero, anakweza dzanja lake nʼkumenya thanthwelo kawiri ndi ndodo yake. Ndiyeno madzi ambiri anayamba kutuluka ndipo gulu lonselo linayamba kumwa madziwo limodzi ndi ziweto zawo.+