Numeri 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pambuyo pake Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Chifukwa simunasonyeze chikhulupiriro mwa ine ndipo simunandilemekeze pamaso pa Aisiraeli, simudzalowetsa mpingowu mʼdziko limene ndidzawapatse.”+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:12 Nsanja ya Olonda,9/1/2009, tsa. 19
12 Pambuyo pake Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Chifukwa simunasonyeze chikhulupiriro mwa ine ndipo simunandilemekeze pamaso pa Aisiraeli, simudzalowetsa mpingowu mʼdziko limene ndidzawapatse.”+