Numeri 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Potsirizira pake, tinalirira Yehova+ ndipo iye anamva kulira kwathu. Iye anatitumizira mngelo+ nʼkutitulutsa mʼdziko la Iguputo. Tsopano tili kuno ku Kadesi, mzinda umene uli mʼmalire a dziko lanu.
16 Potsirizira pake, tinalirira Yehova+ ndipo iye anamva kulira kwathu. Iye anatitumizira mngelo+ nʼkutitulutsa mʼdziko la Iguputo. Tsopano tili kuno ku Kadesi, mzinda umene uli mʼmalire a dziko lanu.