Numeri 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma iye anakanabe kuti: “Ayi, musadzere mʼdziko lathu.”+ Mfumu ya Edomu itanena zimenezi, inatuluka ndi chigulu cha anthu komanso asilikali amphamvu.*
20 Koma iye anakanabe kuti: “Ayi, musadzere mʼdziko lathu.”+ Mfumu ya Edomu itanena zimenezi, inatuluka ndi chigulu cha anthu komanso asilikali amphamvu.*