Numeri 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Aroni aikidwa mʼmanda ngati mmene zinakhalira ndi makolo ake.*+ Iye sadzalowa mʼdziko limene ndidzapatse Aisiraeli chifukwa awirinu munapandukira malangizo anga okhudza madzi a ku Meriba.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:24 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2018, ptsa. 14-15 Nsanja ya Olonda,9/1/2009, tsa. 19
24 “Aroni aikidwa mʼmanda ngati mmene zinakhalira ndi makolo ake.*+ Iye sadzalowa mʼdziko limene ndidzapatse Aisiraeli chifukwa awirinu munapandukira malangizo anga okhudza madzi a ku Meriba.+