Numeri 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfumu ya Akanani ya ku Aradi+ yomwe inkakhala ku Negebu itamva kuti Aisiraeli akubwera kudzera njira ya ku Atarimu, inapita kukamenyana nawo ndipo inagwira Aisiraeli ena nʼkupita nawo kudziko lake.
21 Mfumu ya Akanani ya ku Aradi+ yomwe inkakhala ku Negebu itamva kuti Aisiraeli akubwera kudzera njira ya ku Atarimu, inapita kukamenyana nawo ndipo inagwira Aisiraeli ena nʼkupita nawo kudziko lake.