Numeri 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Yehova anamva mawu a Aisiraeli ndipo anapereka Akananiwo mʼmanja mwawo. Aisiraeli anawononga Akananiwo limodzi ndi mizinda yawo. Nʼchifukwa chake malowo anawatchula kuti Horima.*+
3 Choncho Yehova anamva mawu a Aisiraeli ndipo anapereka Akananiwo mʼmanja mwawo. Aisiraeli anawononga Akananiwo limodzi ndi mizinda yawo. Nʼchifukwa chake malowo anawatchula kuti Horima.*+