Numeri 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene Aisiraeliwo ankapitiriza ulendo wawo kuchokera kuphiri la Hora+ kudzera njira yopita ku Nyanja Yofiira, pofuna kulambalala dziko la Edomu,+ anthuwo anatopa ndi ulendowo. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:4 Nsanja ya Olonda,3/1/1995, tsa. 17
4 Pamene Aisiraeliwo ankapitiriza ulendo wawo kuchokera kuphiri la Hora+ kudzera njira yopita ku Nyanja Yofiira, pofuna kulambalala dziko la Edomu,+ anthuwo anatopa ndi ulendowo.