Numeri 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho anthuwo anapita kwa Mose nʼkumuuza kuti: “Tachimwa ife chifukwa cholankhula modandaula potsutsana ndi Yehova ndiponso inuyo.+ Tipepesereni kwa Yehova kuti atichotsere njokazi.” Zitatero Mose anawapepesera kwa Mulungu.+
7 Choncho anthuwo anapita kwa Mose nʼkumuuza kuti: “Tachimwa ife chifukwa cholankhula modandaula potsutsana ndi Yehova ndiponso inuyo.+ Tipepesereni kwa Yehova kuti atichotsere njokazi.” Zitatero Mose anawapepesera kwa Mulungu.+