Numeri 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Upange chifanizo cha njoka yapoizoni* ndipo uchiike pamtengo. Ndiye munthu aliyense akalumidwa, aziyangʼana chifanizocho kuti akhalebe ndi moyo.”
8 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Upange chifanizo cha njoka yapoizoni* ndipo uchiike pamtengo. Ndiye munthu aliyense akalumidwa, aziyangʼana chifanizocho kuti akhalebe ndi moyo.”