Numeri 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako anasamuka ku Oboti nʼkukamanga msasa ku Iye-abarimu,+ mʼchipululu choyangʼanizana ndi dziko la Mowabu, chakumʼmawa.
11 Kenako anasamuka ku Oboti nʼkukamanga msasa ku Iye-abarimu,+ mʼchipululu choyangʼanizana ndi dziko la Mowabu, chakumʼmawa.