-
Numeri 21:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Atachoka kumeneko anapita ku Beere. Kumeneku ndi kumene kunali chitsime chimene Yehova anauza Mose kuti: “Sonkhanitsa anthuwo kuti ndiwapatse madzi.”
-