-
Numeri 21:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Chitsimechi chinakumbidwa ndi akalonga, chinafukulidwa ndi anthu olemekezeka,
Anachifukula ndi ndodo ya mtsogoleri wa asilikali komanso ndodo zawo.”
Kenako anachoka kuchipululuko nʼkupita ku Matana.
-