Numeri 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Tiloleni tidutse mʼdziko lanu. Sitikhotera mʼmunda uliwonse kapena mʼmunda wa mpesa. Sitimwa madzi pachitsime chilichonse. Tizingoyenda mu Msewu wa Mfumu mpaka titadutsa mʼdziko lanu.”+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:22 ‘Dziko Lokoma’, ptsa. 8-9
22 “Tiloleni tidutse mʼdziko lanu. Sitikhotera mʼmunda uliwonse kapena mʼmunda wa mpesa. Sitimwa madzi pachitsime chilichonse. Tizingoyenda mu Msewu wa Mfumu mpaka titadutsa mʼdziko lanu.”+