Numeri 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako Mose anatumiza anthu ena kuti akazonde mzinda wa Yazeri.+ Atatero, Aisiraeliwo analanda midzi yozungulira mzindawo, nʼkuthamangitsa Aamori amene anali kumeneko.
32 Kenako Mose anatumiza anthu ena kuti akazonde mzinda wa Yazeri.+ Atatero, Aisiraeliwo analanda midzi yozungulira mzindawo, nʼkuthamangitsa Aamori amene anali kumeneko.