Numeri 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho akuluakulu a ku Mowabu ndi a ku Midiyani anapita kwa Balamu+ atatenga ndalama zoti akamulipire kuti awawombezere maula, komanso anamuuza zimene Balaki ananena.
7 Choncho akuluakulu a ku Mowabu ndi a ku Midiyani anapita kwa Balamu+ atatenga ndalama zoti akamulipire kuti awawombezere maula, komanso anamuuza zimene Balaki ananena.