-
Numeri 22:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Balamu anadzuka mʼmamawa nʼkuuza akalonga a Balakiwo kuti: “Pitani kudziko lanu, chifukwa Yehova wakana kuti ndipite nanu.”
-