Numeri 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Potsirizira pake, Yehova anachititsa kuti buluyo alankhule,*+ ndipo anafunsa Balamu kuti: “Kodi ndakulakwirani chiyani kuti mundikwapule katatu konseka?”+
28 Potsirizira pake, Yehova anachititsa kuti buluyo alankhule,*+ ndipo anafunsa Balamu kuti: “Kodi ndakulakwirani chiyani kuti mundikwapule katatu konseka?”+