-
Numeri 22:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Balamu anayankha buluyo kuti: “Chifukwa wandipusitsa kwambiri. Moti ndikanakhala ndi lupanga mʼdzanja langa, bwenzi pano nʼtakupha!”
-