Numeri 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako Yehova anatsegula maso a Balamu,+ ndipo anaona mngelo wa Yehova ataima panjirapo, lupanga lili mʼmanja. Nthawi yomweyo, Balamu anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi.
31 Kenako Yehova anatsegula maso a Balamu,+ ndipo anaona mngelo wa Yehova ataima panjirapo, lupanga lili mʼmanja. Nthawi yomweyo, Balamu anagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yake pansi.