Numeri 22:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndiyeno mngelo wa Yehova uja anamʼfunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani wakhala ukukwapula bulu wako maulendo atatu onsewa? Inetu ndabwera kudzakutchingira njira, chifukwa ukupita kukachita zinthu zotsutsana ndi zimene ine ndikufuna.+
32 Ndiyeno mngelo wa Yehova uja anamʼfunsa kuti: “Nʼchifukwa chiyani wakhala ukukwapula bulu wako maulendo atatu onsewa? Inetu ndabwera kudzakutchingira njira, chifukwa ukupita kukachita zinthu zotsutsana ndi zimene ine ndikufuna.+