-
Numeri 22:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Kumeneko Balaki anapereka nsembe zanyama ya ngʼombe ndi nkhosa, nʼkutumiza ina kwa Balamu ndi akalonga amene anali nawo limodzi.
-